Ekisodo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Usapereke umboni wonamizira mnzako.+ Maliko 14:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Pa nthawiyi ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda* anali kufunafuna umboni kuti amunamizire mlandu Yesu ndi kumupha,+ koma sanali kuupeza.+
55 Pa nthawiyi ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda* anali kufunafuna umboni kuti amunamizire mlandu Yesu ndi kumupha,+ koma sanali kuupeza.+