Maliko 14:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Ndiyeno ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda ankafunafuna umboni kuti anamizire Yesu mlandu nʼcholinga choti amuphe, koma sanaupeze.+
55 Ndiyeno ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda ankafunafuna umboni kuti anamizire Yesu mlandu nʼcholinga choti amuphe, koma sanaupeze.+