Salimo 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu inu, talawani ndipo muona kuti Yehova ndi wabwino.+Wodala ndi munthu wamphamvu amene amathawira kwa iye.+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+
8 Anthu inu, talawani ndipo muona kuti Yehova ndi wabwino.+Wodala ndi munthu wamphamvu amene amathawira kwa iye.+