Salimo 53:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nthawi yomweyo anagwidwa ndi mantha aakulu,+Ngakhale kuti panalibe chochititsa mantha.+Pakuti Mulungu adzamwaza mafupa a aliyense womanga msasa kuti akuukireni.+Isiraeli adzawachititsa manyazi pakuti Yehova wawakana.+
5 Nthawi yomweyo anagwidwa ndi mantha aakulu,+Ngakhale kuti panalibe chochititsa mantha.+Pakuti Mulungu adzamwaza mafupa a aliyense womanga msasa kuti akuukireni.+Isiraeli adzawachititsa manyazi pakuti Yehova wawakana.+