Ezekieli 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Munthu wolungama akasiya chilungamo chake n’kumachita zinthu zopanda chilungamo+ n’kufa chifukwa cha zochita zakezo, wafa chifukwa cha zochita zake zopanda chilungamo.+
26 “‘Munthu wolungama akasiya chilungamo chake n’kumachita zinthu zopanda chilungamo+ n’kufa chifukwa cha zochita zakezo, wafa chifukwa cha zochita zake zopanda chilungamo.+