Deuteronomo 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Iweyo ugona pamodzi ndi makolo ako,+ ndipo anthu awa adzaimirira+ ndi kuchita chiwerewere pakati pawo ndi milungu yachilendo ya m’dziko limene akupita.+ Iwo adzandisiya+ ndi kuphwanya pangano limene ndinapangana nawo.+ Deuteronomo 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo andichititsa nsanje ndi milungu yachabe.+Andisautsa ndi mafano awo opanda pake.+Ndipo ine ndidzawachititsa nsanje ndi anthu achabe,+Ndidzawakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+ 1 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+
16 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Iweyo ugona pamodzi ndi makolo ako,+ ndipo anthu awa adzaimirira+ ndi kuchita chiwerewere pakati pawo ndi milungu yachilendo ya m’dziko limene akupita.+ Iwo adzandisiya+ ndi kuphwanya pangano limene ndinapangana nawo.+
21 Iwo andichititsa nsanje ndi milungu yachabe.+Andisautsa ndi mafano awo opanda pake.+Ndipo ine ndidzawachititsa nsanje ndi anthu achabe,+Ndidzawakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+
4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+