1 Samueli 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Samueli anauza Sauli kuti: “Wachita chinthu chopusa.+ Sunatsatire lamulo+ limene Yehova Mulungu wako anakupatsa.+ Ukanatsatira lamulo limeneli, Yehova akanalimbitsa ufumu wako pa Isiraeli mpaka kalekale. 1 Samueli 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndi kuwawononga+ pamodzi ndi zonse zimene ali nazo. Usakawamvere chisoni, ukawaphe ndithu. Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamng’ono ndi mwana woyamwa,+ ng’ombe ndi nkhosa, ngamila ndi bulu.’”+
13 Pamenepo Samueli anauza Sauli kuti: “Wachita chinthu chopusa.+ Sunatsatire lamulo+ limene Yehova Mulungu wako anakupatsa.+ Ukanatsatira lamulo limeneli, Yehova akanalimbitsa ufumu wako pa Isiraeli mpaka kalekale.
3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndi kuwawononga+ pamodzi ndi zonse zimene ali nazo. Usakawamvere chisoni, ukawaphe ndithu. Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamng’ono ndi mwana woyamwa,+ ng’ombe ndi nkhosa, ngamila ndi bulu.’”+