Ekisodo 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+ Yesaya 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Anthu inu, konzekerani kupha ana ake chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ kuti asalandenso dziko lapansi n’kulidzaza ndi mizinda.”+
5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+
21 “Anthu inu, konzekerani kupha ana ake chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ kuti asalandenso dziko lapansi n’kulidzaza ndi mizinda.”+