Nahumu 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi anthu inu mungakonze chiwembu chotani kuti muukire Yehova?+ Iye adzakufafanizani moti simudzakhalaponso. Sipadzakhalanso nsautso.+
9 Kodi anthu inu mungakonze chiwembu chotani kuti muukire Yehova?+ Iye adzakufafanizani moti simudzakhalaponso. Sipadzakhalanso nsautso.+