Salimo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe,+Ndiponso n’chifukwa chiyani mitundu ya anthu ikung’ung’udza za chinthu chopanda pake?+ Salimo 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti akuchitirani zinthu zoipa.+Alinganiza kuchita zinthu zimene sangazikwanitse.+ Yesaya 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Konzani zochita, koma zidzalephereka.+ Nenani zoti anthu achite, koma sizidzachitidwa, chifukwa Mulungu ali nafe.+
2 N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe,+Ndiponso n’chifukwa chiyani mitundu ya anthu ikung’ung’udza za chinthu chopanda pake?+
10 Konzani zochita, koma zidzalephereka.+ Nenani zoti anthu achite, koma sizidzachitidwa, chifukwa Mulungu ali nafe.+