Ekisodo 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+ Levitiko 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Otsala pakati panu, adzazunzika+ chifukwa cha zolakwa zawo m’mayiko a adani awo. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ mmene makolowo anazunzikira.
5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+
39 Otsala pakati panu, adzazunzika+ chifukwa cha zolakwa zawo m’mayiko a adani awo. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ mmene makolowo anazunzikira.