Deuteronomo 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo kanthu kalikonse koyenera kuwonongedwa* kasamamatire kudzanja lanu,+ kuti mkwiyo woyaka moto wa Yehova usiye kukuyakirani+ ndipo akuchitireni chifundo ndi kukumverani chisoni,+ kutinso akuchulukitseni, monga mmene analumbirira makolo anu.+ Yoswa 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma zinthu zoyenera kuwonongedwa musamale nazo,+ kuopera kuti mungazikhumbire+ n’kutengako zinthuzo,+ n’kuchititsa msasa wa Isiraeli nawonso kukhala chinthu choyenera kuwonongedwa ndi kunyanyalidwa.+
17 Ndipo kanthu kalikonse koyenera kuwonongedwa* kasamamatire kudzanja lanu,+ kuti mkwiyo woyaka moto wa Yehova usiye kukuyakirani+ ndipo akuchitireni chifundo ndi kukumverani chisoni,+ kutinso akuchulukitseni, monga mmene analumbirira makolo anu.+
18 Koma zinthu zoyenera kuwonongedwa musamale nazo,+ kuopera kuti mungazikhumbire+ n’kutengako zinthuzo,+ n’kuchititsa msasa wa Isiraeli nawonso kukhala chinthu choyenera kuwonongedwa ndi kunyanyalidwa.+