1 Samueli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho utsogole kupita ku Giligala.+ Inenso ndipita kumeneko kuti ndikapereke nsembe zopsereza ndi kupereka nsembe zachiyanjano.+ Ukandidikire masiku 7+ mpaka nditakupeza, ndipo ndikadzafika ndidzakuuza zoti uchite.” 1 Samueli 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndikumva chisoni+ kuti ndinaika Sauli kukhala mfumu. Iye watembenuka,+ wasiya kunditsatira, ndipo sakumvera mawu anga.”+ Samueli anavutika maganizo kwambiri ndi nkhani imeneyi+ moti anafuulira Yehova usiku wonse.+
8 Choncho utsogole kupita ku Giligala.+ Inenso ndipita kumeneko kuti ndikapereke nsembe zopsereza ndi kupereka nsembe zachiyanjano.+ Ukandidikire masiku 7+ mpaka nditakupeza, ndipo ndikadzafika ndidzakuuza zoti uchite.”
11 “Ndikumva chisoni+ kuti ndinaika Sauli kukhala mfumu. Iye watembenuka,+ wasiya kunditsatira, ndipo sakumvera mawu anga.”+ Samueli anavutika maganizo kwambiri ndi nkhani imeneyi+ moti anafuulira Yehova usiku wonse.+