Genesis 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero, Yehova anamva chisoni+ kuti anapanga anthu padziko lapansi, ndipo zinam’pweteka kwambiri mumtima.+ 1 Samueli 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Samueli anamuyankha kuti: “Sindibwerera nawe chifukwa wakana mawu a Yehova, ndipo Yehova wakukana kuti upitirize kukhala mfumu ya Isiraeli.”+ 1 Samueli 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Samueli analirira+ Sauli ndipo sanaonanenso naye mpaka tsiku la imfa yake. Koma Yehova anamva chisoni kuti anaika Sauli kukhala mfumu ya Isiraeli.+ Yeremiya 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ndiyeno anthuwo n’kusiya zoipa zimene anali kuchita, zimene ndinawadzudzula nazo,+ pamenepo ndidzasintha maganizo anga kuti ndisawagwetsere tsoka limene ndinafuna kuwagwetsera.+
6 Chotero, Yehova anamva chisoni+ kuti anapanga anthu padziko lapansi, ndipo zinam’pweteka kwambiri mumtima.+
26 Samueli anamuyankha kuti: “Sindibwerera nawe chifukwa wakana mawu a Yehova, ndipo Yehova wakukana kuti upitirize kukhala mfumu ya Isiraeli.”+
35 Samueli analirira+ Sauli ndipo sanaonanenso naye mpaka tsiku la imfa yake. Koma Yehova anamva chisoni kuti anaika Sauli kukhala mfumu ya Isiraeli.+
8 ndiyeno anthuwo n’kusiya zoipa zimene anali kuchita, zimene ndinawadzudzula nazo,+ pamenepo ndidzasintha maganizo anga kuti ndisawagwetsere tsoka limene ndinafuna kuwagwetsera.+