-
Yona 4:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Choncho iye anapemphera kwa Yehova kuti: “Inu Yehova, kodi zimene ndimaopa ndili kwathu zija si zimenezi? N’chifukwa chaketu ine ndinathawa kupita ku Tarisi.+ Ndinadziwa kuti inu ndinu Mulungu wachisomo ndi wachifundo,+ wosakwiya msanga, wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ komanso mumatha kusintha maganizo pa tsoka limene mumafuna kubweretsa.+
-