Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Sambani,+ dziyeretseni.+ Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.+ Lekani kuchita zoipa.+

  • Yesaya 55:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+

  • Yeremiya 36:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mwina anthu a m’nyumba ya Yuda adzamva za masoka onse amene ndikufuna kuwagwetsera+ ndipo aliyense abwerera ndi kusiya njira yake yoipa.+ Akatero, ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndi machimo awo.”+

  • Ezekieli 18:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “‘Munthu woipa akasiya zinthu zoipa zimene anali kuchita n’kumachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ iyeyu adzapulumutsa moyo wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena