Salimo 78:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Iwo analitu kumupandukira kawirikawiri m’chipululu,+Anali kumukhumudwitsa m’chipululumo!+ Salimo 95:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kwa zaka 40, m’badwo umenewo unali kundinyansa,+Ndipo ndinati:“Anthu awa mitima yawo imasochera,+Ndipo sadziwa njira zanga.”+
10 Kwa zaka 40, m’badwo umenewo unali kundinyansa,+Ndipo ndinati:“Anthu awa mitima yawo imasochera,+Ndipo sadziwa njira zanga.”+