Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 “Anthu anu Aisiraeli akagonja kwa adani+ awo chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno akabwerera kwa inu+ n’kutamanda dzina lanu+ ndi kupemphera+ ndiponso kupempha kwa inu kuti muwachitire chifundo m’nyumba ino,+

  • Yeremiya 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Konzani njira zanu ndiponso zochita zanu kuti zikhale zabwino, ndipo ndidzachititsa anthu inu kukhalabe m’dziko lino.+

  • Ezekieli 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “‘Munthu woipa akabwerera, kusiya machimo ake onse amene anali kuchita+ ndipo akasunga malamulo anga onse n’kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ adzakhalabe ndi moyo. Sadzafa ayi.+

  • Ezekieli 33:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Auze kuti, ‘“Pali ine Mulungu wamoyo,” watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, “Ine sindisangalala ndi imfa ya munthu woipa,+ koma ndimafuna kuti munthu woipa abwerere+ kusiya njira zake n’kukhala ndi moyo.+ Bwererani! Bwererani ndi kusiya njira zanu zoipa.+ Muferenji inu a nyumba ya Isiraeli?”’+

  • Yona 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Anthu a ku Nineve anayamba kukhulupirira Mulungu+ ndipo anayamba kulengeza kuti aliyense, popanda wotsala, asale kudya ndipo avale ziguduli.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena