Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tonsefe tidzafa+ ndi kukhala ngati madzi otayika amene sawoleka. Koma Mulungu wakonza zinthu+ ndipo ali ndi zifukwa zothandiza kuti munthu wopitikitsidwa asapitirize kukhala wopitikitsidwa.

  • Ezekieli 18:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “‘Kodi ine ndimasangalala ndi imfa ya munthu aliyense wochimwa?+ Kodi sindisangalala kuti munthu wochimwayo abwerere kusiya njira zakezo ndi kukhalabe ndi moyo?’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

  • Luka 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho ndikukuuzani, kumakhala chisangalalo chochuluka kwa angelo a Mulungu chifukwa cha munthu mmodzi wochimwa amene walapa.”+

  • 1 Timoteyo 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 amene chifuniro chake n’chakuti anthu, kaya akhale a mtundu wotani,+ apulumuke+ ndi kukhala odziwa choonadi+ molondola.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena