Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mverani kudzudzula kwanga ndipo mubwerere.+ Mukatero ndidzachititsa kuti mzimu wanga usefukire kwa inu+ ndipo ndidzakudziwitsani mawu anga.+

  • Yesaya 55:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+

  • Yeremiya 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Bwererani, inu ana opanduka.+ Ndidzachiritsa kusakhulupirika kwanu.”+

      “Ife tabwerera! Tabwera kwa inu, pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+

  • Yeremiya 25:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Aneneriwo anali kukuuzani kuti, ‘Chonde, aliyense wa inu atembenuke ndi kusiya njira yake yoipa ndi zochita zake zoipa+ kuti mupitirize kukhala m’dziko limene Yehova anakupatsani, inuyo ndi makolo anu. Anakupatsani dzikoli kuti chikhale cholowa chanu kwa nthawi yaitali.+

  • Ezekieli 14:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Choncho uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Bwererani, siyani mafano anu onyansa.+ Tembenuzani nkhope zanu kuti musayang’anenso zinthu zanu zonse zonyansa.+

  • Hoseya 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Iwe Isiraeli, bwerera kwa Yehova Mulungu wako+ pakuti wapunthwa mu zolakwa zako.+

  • Machitidwe 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Chotero lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa+ zibwere kuchokera kwa Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena