Yesaya 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zophimbira mafano anu ogoba asiliva ndi zokutira zifaniziro zanu zopangidwa ndi golide+ wosungunula,+ mudzaziona kuti ndi zonyansa+ ndipo mudzazitaya.+ Monga mkazi amene akusamba yemwe amataya monyansidwa kansalu kake, mudzanena kuti: “Nyansi zimenezi!”+ Yeremiya 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chigololo chako,+ kumemesa* kwako,+ khalidwe lako lotayirira la uhule, zonsezi zidzaonekera. Ndaona zinthu zako zonyansa pamapiri kuthengo.+ Tsoka kwa iwe Yerusalemu! Sungakhale woyera.+ Kodi udzakhalabe wosayera kufikira liti?”+
22 Zophimbira mafano anu ogoba asiliva ndi zokutira zifaniziro zanu zopangidwa ndi golide+ wosungunula,+ mudzaziona kuti ndi zonyansa+ ndipo mudzazitaya.+ Monga mkazi amene akusamba yemwe amataya monyansidwa kansalu kake, mudzanena kuti: “Nyansi zimenezi!”+
27 Chigololo chako,+ kumemesa* kwako,+ khalidwe lako lotayirira la uhule, zonsezi zidzaonekera. Ndaona zinthu zako zonyansa pamapiri kuthengo.+ Tsoka kwa iwe Yerusalemu! Sungakhale woyera.+ Kodi udzakhalabe wosayera kufikira liti?”+