Miyambo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsoka limatsatira ochimwa,+ koma olungama ndi amene amalandira mphoto zabwino.+ Mlaliki 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usakhale woipa mopitirira muyezo,+ komanso usakhale wopusa.+ Uferenji mwamsanga?+ Yeremiya 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinati: “Ndithudi, amenewa ndi anthu onyozeka. Anachita zinthu mopusa, pakuti anakana njira ya Yehova. Anakana chilamulo cha Mulungu wawo.+
4 Ine ndinati: “Ndithudi, amenewa ndi anthu onyozeka. Anachita zinthu mopusa, pakuti anakana njira ya Yehova. Anakana chilamulo cha Mulungu wawo.+