Miyambo 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Woipa adzakankhidwa chifukwa cha kuipa kwake,+ koma wolungama adzapeza malo othawirako chifukwa cha mtima wake wosagawanika.+ Miyambo 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu wochoka pa njira yochita zinthu mozindikira,+ adzapumula mumpingo wa anthu akufa.+
32 Woipa adzakankhidwa chifukwa cha kuipa kwake,+ koma wolungama adzapeza malo othawirako chifukwa cha mtima wake wosagawanika.+