Yobu 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gawo la munthu woipa lochokera kwa Mulungu,+Zomwe adzalandire kwa Wamphamvuyonse monga cholowa cha ozunza anzawo, ndi izi: Yobu 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zoopsa zadzidzidzi zidzam’tenga ngati madzi.+Usiku chimphepo chamkuntho chidzamuba ndithu. Salimo 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti anthu oipa adzatheratu onse,+Ndipo adani a Yehova adzafanana ndi busa la msipu wobiriwira mochititsa kaso.Iwo adzatha.+ Adzazimiririka ndi kusanduka utsi.+ 1 Atesalonika 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene azidzati:+ “Bata ndi mtendere!”+ chiwonongeko+ chodzidzimutsa chidzafika pa iwo nthawi yomweyo monga zowawa za pobereka za mkazi wapakati,+ ndipo sadzapulumuka.+
13 Gawo la munthu woipa lochokera kwa Mulungu,+Zomwe adzalandire kwa Wamphamvuyonse monga cholowa cha ozunza anzawo, ndi izi:
20 Pakuti anthu oipa adzatheratu onse,+Ndipo adani a Yehova adzafanana ndi busa la msipu wobiriwira mochititsa kaso.Iwo adzatha.+ Adzazimiririka ndi kusanduka utsi.+
3 Pamene azidzati:+ “Bata ndi mtendere!”+ chiwonongeko+ chodzidzimutsa chidzafika pa iwo nthawi yomweyo monga zowawa za pobereka za mkazi wapakati,+ ndipo sadzapulumuka.+