Salimo 76:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene Mulungu ananyamuka ndi kupereka chiweruzo,+Kuti apulumutse anthu onse ofatsa padziko lapansi.+ [Seʹlah.] Salimo 103:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova akuchitira chilungamo+Ndi kuperekera zigamulo anthu amene akuchitiridwa zachinyengo.+
9 Pamene Mulungu ananyamuka ndi kupereka chiweruzo,+Kuti apulumutse anthu onse ofatsa padziko lapansi.+ [Seʹlah.]