Salimo 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Weruzani mlandu wanga inu Yehova, motsutsana ndi adani anga.+Menyani nkhondo ndi kugonjetsa amene akumenyana ndi ine.+ Salimo 94:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nyamukani inu Woweruza dziko lapansi.+Perekani chilango kwa anthu odzikweza.+ Yesaya 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wati: “Tsopano ndinyamuka,+ ndidzikweza.+ Tsopano ndidziika pamwamba.+
35 Weruzani mlandu wanga inu Yehova, motsutsana ndi adani anga.+Menyani nkhondo ndi kugonjetsa amene akumenyana ndi ine.+