Genesis 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+ Salimo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nyamukani, inu Yehova, mu mkwiyo wanu.+Imirirani ndi kukhaulitsa amene andisonyeza mkwiyo ndi kundichitira zoipa.+Dzukani ndi kundithandiza,+ pakuti mwalamula kuti chiweruzo chiperekedwe.+ Salimo 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo kumwamba kukunena za chilungamo chake,+Pakuti Mulungu ndiye Woweruza.+ [Seʹlah.] Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.” Aroma 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiwe ndani kuti uweruze wantchito wapakhomo wa mnzako?+ Ndi udindo wa bwana wake kumuweruza kuti ndi wolakwa kapena wosalakwa.+ Komatu Yehova akhoza kumukomera mtima chifukwa angathe kumuthandiza.+
25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+
6 Nyamukani, inu Yehova, mu mkwiyo wanu.+Imirirani ndi kukhaulitsa amene andisonyeza mkwiyo ndi kundichitira zoipa.+Dzukani ndi kundithandiza,+ pakuti mwalamula kuti chiweruzo chiperekedwe.+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”
4 Ndiwe ndani kuti uweruze wantchito wapakhomo wa mnzako?+ Ndi udindo wa bwana wake kumuweruza kuti ndi wolakwa kapena wosalakwa.+ Komatu Yehova akhoza kumukomera mtima chifukwa angathe kumuthandiza.+