2 Mafumu 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtumiki+ wa munthu wa Mulungu woona atadzuka m’mawa n’kutuluka panja, anangoona kuti gulu lankhondo lazungulira mzindawo ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo. Nthawi yomweyo mtumikiyo anadandaulira mbuye wake kuti: “Kalanga ine mbuyanga!+ Titani?” Yeremiya 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ine ndikudziwa bwino, inu Yehova, kuti munthu wochokera kufumbi alibe ulamuliro wowongolera njira ya moyo wake. Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake.+
15 Mtumiki+ wa munthu wa Mulungu woona atadzuka m’mawa n’kutuluka panja, anangoona kuti gulu lankhondo lazungulira mzindawo ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo. Nthawi yomweyo mtumikiyo anadandaulira mbuye wake kuti: “Kalanga ine mbuyanga!+ Titani?”
23 Ine ndikudziwa bwino, inu Yehova, kuti munthu wochokera kufumbi alibe ulamuliro wowongolera njira ya moyo wake. Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake.+