Salimo 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapazi anga ayendebe m’njira zanu,+Mmene sadzapunthwa ngakhale pang’ono.+ Salimo 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova walimbitsa mapazi a munthu wamphamvu zake,+Ndipo Mulungu amakondwera ndi njira zake.+ Miyambo 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pereka ntchito zako kwa Yehova,+ ndipo zolinga zako ndithu zidzakhazikika.+ Miyambo 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mayendedwe a mwamuna wamphamvu amachokera kwa Yehova,+ koma kodi munthu wochokera kufumbi angazindikire bwanji njira yake?+ Yeremiya 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Mtima ndi wonyenga kwambiri kuposa china chilichonse ndipo ungathe kuchita china chilichonse choipa.*+ Ndani angaudziwe?
24 Mayendedwe a mwamuna wamphamvu amachokera kwa Yehova,+ koma kodi munthu wochokera kufumbi angazindikire bwanji njira yake?+
9 “Mtima ndi wonyenga kwambiri kuposa china chilichonse ndipo ungathe kuchita china chilichonse choipa.*+ Ndani angaudziwe?