Salimo 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano munthu woopa Yehova ndani?+Adzamulangiza kuyenda m’njira imene adzasankha.+ Miyambo 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nzeru za munthu wochenjera ndizo kuzindikira njira imene akuyendamo,+ koma kuganiza mopusa kwa zitsiru ndi chinyengo.+ Miyambo 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu angaganize za njira zake mumtima mwake,+ koma Yehova ndiye amawongolera mayendedwe ake.+
8 Nzeru za munthu wochenjera ndizo kuzindikira njira imene akuyendamo,+ koma kuganiza mopusa kwa zitsiru ndi chinyengo.+