Salimo 111:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chiyambi cha nzeru ndicho kuopa Yehova.+ ש [Sin]Onse otsatira malamulo a Mulungu ndi ozindikira.+ ת [Taw]Iye ayenera kutamandidwa mpaka muyaya.+ Machitidwe 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iyeyu anali wopembedza+ ndi woopa+ Mulungu pamodzi ndi banja lake lonse. Anali kupatsa anthu mphatso zambiri zachifundo+ ndipo anali kupemphera kwa Mulungu nthawi zonse.+
10 Chiyambi cha nzeru ndicho kuopa Yehova.+ ש [Sin]Onse otsatira malamulo a Mulungu ndi ozindikira.+ ת [Taw]Iye ayenera kutamandidwa mpaka muyaya.+
2 Iyeyu anali wopembedza+ ndi woopa+ Mulungu pamodzi ndi banja lake lonse. Anali kupatsa anthu mphatso zambiri zachifundo+ ndipo anali kupemphera kwa Mulungu nthawi zonse.+