Salimo 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova walimbitsa mapazi a munthu wamphamvu zake,+Ndipo Mulungu amakondwera ndi njira zake.+ Yeremiya 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ine ndikudziwa bwino, inu Yehova, kuti munthu wochokera kufumbi alibe ulamuliro wowongolera njira ya moyo wake. Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake.+
23 Ine ndikudziwa bwino, inu Yehova, kuti munthu wochokera kufumbi alibe ulamuliro wowongolera njira ya moyo wake. Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake.+