Salimo 18:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mudzakulitsa malo opondapo mapazi anga,+Ndipo mapazi anga sadzagwedezeka.+ Salimo 94:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa literereka,”+Kukoma mtima kwanu kosatha, inu Yehova, kunandichirikiza.+ Salimo 121:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sangalole kuti phazi lako lipunthwe.+Amene amakuyang’anira sangawodzere.+
18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa literereka,”+Kukoma mtima kwanu kosatha, inu Yehova, kunandichirikiza.+