1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+ Salimo 119:133 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 133 Mwapondetsa mwamphamvu mapazi anga pa mawu anu,+Ndipo musalole kuti choipa chilichonse chindilamulire.+
9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+
133 Mwapondetsa mwamphamvu mapazi anga pa mawu anu,+Ndipo musalole kuti choipa chilichonse chindilamulire.+