Salimo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso mundiletse kuchita modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+Pamenepo ndidzakhala wopanda chifukwa,+Ndipo ndidzakhalabe wopanda milandu yambiri yophwanya malamulo. Aroma 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe monga mfumu+ m’matupi anu okhoza kufawo kuti muzitsatira zilakolako zawo.+
13 Komanso mundiletse kuchita modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+Pamenepo ndidzakhala wopanda chifukwa,+Ndipo ndidzakhalabe wopanda milandu yambiri yophwanya malamulo.
12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe monga mfumu+ m’matupi anu okhoza kufawo kuti muzitsatira zilakolako zawo.+