Genesis 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ukasintha n’kuchita chabwino, sindikuyanja kodi?+ Koma ngati susintha kuti uchite chabwino, uchimo wamyata pakhomo kukudikirira, ndipo ukulakalaka kukudya.+ Kodi iweyo suugonjetsa?”+ Salimo 119:133 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 133 Mwapondetsa mwamphamvu mapazi anga pa mawu anu,+Ndipo musalole kuti choipa chilichonse chindilamulire.+
7 Ukasintha n’kuchita chabwino, sindikuyanja kodi?+ Koma ngati susintha kuti uchite chabwino, uchimo wamyata pakhomo kukudikirira, ndipo ukulakalaka kukudya.+ Kodi iweyo suugonjetsa?”+
133 Mwapondetsa mwamphamvu mapazi anga pa mawu anu,+Ndipo musalole kuti choipa chilichonse chindilamulire.+