Salimo 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+ Salimo 119:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Ndisanagwe m’masautso ndinali kuchimwa mosadziwa,+Koma tsopano ndimasunga mawu anu.+
30 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+