Salimo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka. Salimo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+ Salimo 119:140 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 140 Mawu anu ndi oyengeka kwambiri,+Ndipo ine mtumiki wanu ndimawakonda.+
6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka.
8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+