2 Samueli 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+ Salimo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka. Salimo 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+ Salimo 119:160 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo chigamulo chanu chilichonse cholungama chidzakhalapo mpaka kalekale.+ Miyambo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu alionse a Mulungu ndi oyera.+ Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+ Yohane 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ayeretseni+ ndi choonadi. Mawu+ anu ndiwo choonadi.+
31 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+
6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka.
30 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+
160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo chigamulo chanu chilichonse cholungama chidzakhalapo mpaka kalekale.+