2 Samueli 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+ Salimo 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+ Salimo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+ Salimo 119:140 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 140 Mawu anu ndi oyengeka kwambiri,+Ndipo ine mtumiki wanu ndimawakonda.+ Miyambo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu alionse a Mulungu ndi oyera.+ Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+
31 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+
30 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+
8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+