Miyambo 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kulungama kwa anthu owongoka mtima n’kumene kudzawapulumutse,+ koma anthu ochita zinthu mwachinyengo adzagwidwa ndi zolakalaka zawo.+ Yakobo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu aliyense amayesedwa mwa kukopedwa ndi kukodwa m’chilakolako chake.+
6 Kulungama kwa anthu owongoka mtima n’kumene kudzawapulumutse,+ koma anthu ochita zinthu mwachinyengo adzagwidwa ndi zolakalaka zawo.+