Mlaliki 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+ Ezekieli 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Munthu woipa akasiya zinthu zoipa zimene anali kuchita n’kumachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ iyeyu adzapulumutsa moyo wake.+
13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+
27 “‘Munthu woipa akasiya zinthu zoipa zimene anali kuchita n’kumachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ iyeyu adzapulumutsa moyo wake.+