1 Mafumu 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Asa anachita zabwino pamaso pa Yehova monga anachitira Davide kholo lake.+ 2 Mbiri 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anachotsa malo okwezeka ndi maguwa ofukizirapo zonunkhira+ m’mizinda yonse ya Yuda, ndipo ufumuwo unapitiriza kukhala wopanda chosokoneza chilichonse+ mu ulamuliro wake.
5 Iye anachotsa malo okwezeka ndi maguwa ofukizirapo zonunkhira+ m’mizinda yonse ya Yuda, ndipo ufumuwo unapitiriza kukhala wopanda chosokoneza chilichonse+ mu ulamuliro wake.