2 Mafumu 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu onse a m’dzikolo anapitiriza kusangalala,+ ndipo mumzindawo munali bata. Ataliya anali atamupha ndi lupanga panyumba ya mfumu.+
20 Anthu onse a m’dzikolo anapitiriza kusangalala,+ ndipo mumzindawo munali bata. Ataliya anali atamupha ndi lupanga panyumba ya mfumu.+