Ekisodo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+ Deuteronomo 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo munati, ‘Yehova Mulungu wathu watisonyezatu ulemerero wake ndi ukulu wake, ndipo tamva mawu ake kuchokera pakati pa moto.+ Lero taona kuti Mulungu angalankhule ndi munthu, munthuyo n’kukhalabe ndi moyo.+
18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+
24 Pamenepo munati, ‘Yehova Mulungu wathu watisonyezatu ulemerero wake ndi ukulu wake, ndipo tamva mawu ake kuchokera pakati pa moto.+ Lero taona kuti Mulungu angalankhule ndi munthu, munthuyo n’kukhalabe ndi moyo.+