Ekisodo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+ Ekisodo 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kwa ana a Isiraeli, ulemerero wa Yehova unali kuoneka ngati moto wolilima+ pamwamba pa phiri. Deuteronomo 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anakuchititsani kumva mawu ake kuchokera kumwamba n’cholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuona moto wake woopsa, ndipo munamva mawu ake kuchokera pakati pa moto.+
18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+
36 Anakuchititsani kumva mawu ake kuchokera kumwamba n’cholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuona moto wake woopsa, ndipo munamva mawu ake kuchokera pakati pa moto.+