Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako mngelo wa Yehova anaonekera kwa iye pakati pa chitsamba chaminga+ chimene chinali kuyaka moto. Atachiyang’anitsitsa, anaona kuti chitsamba chamingacho chikuyaka, koma sichikupsa.

  • Deuteronomo 4:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.*+

  • Ezekieli 1:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndinaona chinachake chowala ngati siliva wosakanikirana ndi golide,+ chooneka ngati kuti mkati mwake monse mukuyaka moto.+ Kuchokera pa chimene chinali kuoneka ngati chiuno chake kupita m’mwamba ndiponso kutsika m’munsi, munthuyo anali kuoneka ngati moto, ndipo pamalo onse omuzungulira panali powala.

  • Aheberi 12:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pakuti Mulungu wathu alinso moto wowononga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena