Salimo 77:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Madzi akuonani, inu Mulungu,Madzi akuonani, ndipo ayamba kumva ululu woopsa.+Komanso madzi akuya ayamba kuwinduka.+ Salimo 93:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mitsinje ikufuula.Ikufuula ndi mawu amphamvu.+Mitsinje ikupitiriza kufuula ndi mawu amkokomo.+ Salimo 98:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyanja ndi zonse zili mmenemo zichite mkokomo,+Chimodzimodzinso mtunda ndi zonse zokhala kumeneko.+
16 Madzi akuonani, inu Mulungu,Madzi akuonani, ndipo ayamba kumva ululu woopsa.+Komanso madzi akuya ayamba kuwinduka.+
3 Inu Yehova, mitsinje ikufuula.Ikufuula ndi mawu amphamvu.+Mitsinje ikupitiriza kufuula ndi mawu amkokomo.+
7 Nyanja ndi zonse zili mmenemo zichite mkokomo,+Chimodzimodzinso mtunda ndi zonse zokhala kumeneko.+