Yeremiya 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndidzakuimbani mlandu+ mogwirizana ndi zipatso za ntchito zanu,’+ watero Yehova. ‘Ndidzayatsanso moto m’nkhalango za mzindawu,+ moti udzanyeketsa zinthu zonse zouzungulira.’”+ Maliro 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wasonyeza ukali wake wonse.+ Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+Iye wayatsa moto m’Ziyoni, umene wanyeketsa maziko ake.+ Amosi 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzatumiza moto+ panyumba ya Hazaeli,+ ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Beni-hadadi.+
14 ndidzakuimbani mlandu+ mogwirizana ndi zipatso za ntchito zanu,’+ watero Yehova. ‘Ndidzayatsanso moto m’nkhalango za mzindawu,+ moti udzanyeketsa zinthu zonse zouzungulira.’”+
11 Yehova wasonyeza ukali wake wonse.+ Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+Iye wayatsa moto m’Ziyoni, umene wanyeketsa maziko ake.+