Ezekieli 20:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Anthu onse adzaona kuti ine Yehova ndayatsa nkhalangoyo ndi moto ndipo sudzazimitsidwa.”’”+